2 Samuel 1:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Davide adaimba nyimbo ya madandaulo, kulira Saulo ndi Yonatani mwana wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide analirira Saulo ndi Yonatani mwana wake ndi nyimbo iyi ya maliro;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anayimba nyimbo iyi ya maliro, kulira Sauli ndi mwana wake Yonatani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide analirira Sauli ndi Jonatani mwana wace ndi nyimbo iyi ya maliro;