2 Samuel 1:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musakanene zimenezi ku Gati, musakalengeze m'miseu ya ku Asikeloni, kuti akazi a Afilisti angasekerere, akazi a anthu osaumbalidwa angakondwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usachinene ku Gati, usachibukitse m'makwalala a Asikeloni, kuti ana akazi a Afilisti angasekere, kuti ana akazi a osadulidwawo angafuule mokondwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Musakanene zimenezi ku Gati, musazilengeze ku misewu ya ku Asikeloni, kuti ana aakazi a Afilisti angasangalale, ana aakazi a osachita mdulidwe angakondwere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usacinene ku Gati, Usacibukitse m'makwalala a Asikeloni, Kuti ana akazi a Afilisti angasekere, Kuti ana akazi a osadulidwawo angapfuule mokondwera.