2 Samuel 1:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Saulo atacheuka nandiwona, adandiitana. Ndidavomera kuti, ‘Ŵaŵa.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye pakucheukira m'mbuyo mwake anandiona, nandiitana. Ndipo ndinayankha, Ndine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene anatembenuka ndi kundiona ine, iye anandiyitana, ndipo ndinati, ‘Kodi ndichite chiyani?’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye pakuceukira m'mbuyo mwace anandiona, nanditana. Ndipo ndinayankha, Ndine.