2 Samuel 1:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adandifunsa kuti, ‘Ndiwe yani?’ Ine ndidati, ‘Ndine Mwamaleke.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanena, Ndiwe yani? Ndipo ndinayankha kuti, Ndine Mwamaleke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anandifunsa, “Iwe ndiwe yani?” Ine ndinayankha kuti, “Ndine Mwamaleki.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanena, Ndiwe yani? Ndipo ndinayankha kuti, Ndine M-amaleki.