2 Samuel 10:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Asiriya ataona kuti agonjetsedwa ndi Aisraele, adasonkanitsa ankhondo ao onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Aaramu anaona kuti Aisraele anawathyola, anasonkhana pamodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aaramu ataona kuti agonjetsedwa ndi Aisraeli, anasonkhananso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Aaramu anaona kuti Aisrayeli anawathyola, anasonkhana pamodzi.