2 Samuel 10:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide atamva zimenezo, adatuma Yowabu ndi gulu lake lonse la ankhondo, amphamvu okhaokha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Davide anachimva, anatumiza Yowabu ndi khamu lonse la anthu amphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide atamva zimenezi, anatumiza Yowabu ndi gulu lonse la ankhondo amphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Davide anacimva, anatumiza Yoabu ndi khamu lonse la anthu amphamvu.