2 Samuel 11:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene mkazi wa Uriya adamva kuti mwamuna wake Uriya adaphedwa, adalira, kulira mwamuna wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene mkazi wa Uriya anamva kuti Uriya mwamuna wake adamwalira, iye analira maliro a mwamuna wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkazi wa Uriya atamva kuti mwamuna wake wafa, analira maliro.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene mkazi wa Uriya anamva kuti Uriya mwamuna wace adamwalira, iye analira maliro a mwamuna wace.