2 Samuel 12:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake tsono nkhondo siidzachoka pabanja pako chifukwa wandinyoza Ine, ndipo wakwatira mkazi wa Uriya Muhiti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake tsono lupanga silidzachoka pa nyumba yako nthawi zonse, popeza unandipeputsa Ine, nudzitengera mkazi wa Uriya Muhiti akhale mkazi wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo tsopano lupanga silidzachoka pa nyumba yako, chifukwa unandinyoza ine ndi kutenga mkazi wa Uriya Mhiti kukhala wako.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace tsono lupanga silidzacoka pa nyumba yako nthawi zonse, popeza unandipeputsa Ine, nudzitengera mkazi wa Uriya Mhiti akhale mkazi wako.