2 Samuel 12:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe, popeza kuti pochita zimenezi mwanyoza Chauta kotheratu, mwana amene akubalireniyo adzafa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma popeza pakuchita ichi munapatsa chifukwa chachikulu kwa adani a Yehova cha kuchitira mwano, mwanayonso wobadwira inu adzafa ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe, popeza pochita zimenezi mwachititsa kuti adani a Yehova amunyoze, mwana amene akubalireniyo adzafa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma popeza pakucita ici munapatsa cifukwa cacikuru kwa adani a Yehova ca kucitira mwano, mwanayonso wobadwira inu adzafa ndithu.