2 Samuel 12:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Davide adatonthoza mtima wa mkazi wake Bateseba, nakaloŵa kwa mkaziyo. Pambuyo pake mkazi uja adabala mwana wamwamuna, ndipo Davide adamutcha dzina lake Solomoni. Chauta adamkonda mwanayo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anasangalatsa Bateseba mkazi wake, nalowa kwa iye, nagona naye; ndipo anabala mwana wamwamuna, namutcha dzina lake Solomoni. Ndipo Yehova anamkonda iye,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Davide anatonthoza mkazi wake Batiseba, napita kwa iye ndi kugona naye. Iye anabereka mwana wamwamuna, ndipo anamutcha dzina lake Solomoni. Yehova ankamukonda iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anasangalatsa Bateseba mkazi wace, nalowa kwa iye, nagona naye; ndipo anabala mwana wamwamuna, namucha dzina lace Solomo. Ndipo Yehova anamkonda iye,