2 Samuel 12:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo adatumiza mau kudzera mwa mneneri Natani kuti mwanayo dzina lake likhale Yedidiya, chifukwa Chauta adaamkonda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
natumiza ndi dzanja la Natani mneneriyo, namutcha dzina lake Wokondedwa ndi Yehova, chifukwa cha Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo chifukwa chakuti Yehova ankamukonda iyeyo, Yehovayo anatumiza mawu kwa mneneri Natani kuti akamutchule Yedidiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
natumiza ndi dzanja la Natani mneneriyo, namucha dzina lace Wokondedwa ndi Yehova, cifukwa ca Yehova.