2 Samuel 12:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adauza Natani kuti, “Pali Chauta wamoyo, munthu amene adachita zimeneziyu, ayenera kuphedwa basi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mkwiyo wa Davide unayaka ndithu pa munthuyo, nati kwa Natani, Pali Yehova, munthu amene anachita ichi, ayenera kumupha;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anapsa mtima kwambiri chifukwa cha munthuyo ndipo anati kwa Natani, “Pali Yehova, munthu amene anachita zimenezi ayenera kufa basi!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mkwiyo wa Davide unayaka ndithu pa munthuyo, nati kwa Natani, Pali Yehova, munthu amene anacita ici, ayenera kumupha;