2 Samuel 12:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo pa mwanawankhosayo abwezere ena anai, chifukwa chochita zotere, ndiponso popeza kuti analibe chifundo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo adzabwezera mwa mwanawankhosayo ena anai, chifukwa anachita ichi osakhala nacho chifundo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye ayenera kulipira mwana wankhosa wamkaziyo kanayi, chifukwa anachita chinthu chimenechi ndipo analibe chifundo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo adzabwezera mwa mwana wa nkhosayo ena anai, cifukwa anacita ici osakhala naco cifundo.