2 Samuel 13:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Aminoni sadamve zimene ankanena Tamarazo. Ndipo popeza kuti anali ndi mphamvu zoposa Tamara, Aminoniyo adamkakamiza Tamarayo nagona naye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iye sadafuna kumvera mau ake, ndipo popeza anali wamphamvu ndi iye, anamkakamiza, nagona naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma sanamvere zimene amanena Tamara ndipo popeza anali wamphamvu kuposa Tamarayo, iye anamugwirira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye sadafuna kumvera mau ace, ndipo popeza anali wamphamvu ndi iye, anamkangamiza, nagona naye.