2 Samuel 13:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapita kwa mfumu nati, “Amfumu, ine mtumiki wanu ndikukachita ntchito yometa nkhosa ndi anthu anga. Ndimati ngati nkotheka mudzakhale nafe inuyo amfumu pamodzi ndi atumiki anu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Abisalomu nafika kwa mfumu nati, Onani, ine mnyamata wanu ndili nao osenga nkhosa; inu mfumu ndi anyamata anu mupite nane mnyamata wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abisalomu anapita kwa mfumu ndipo anati, “Ometa nkhosa za mtumiki wanu anabwera. Chonde mfumu ndi akuluakulu anu mubwere kudzakhala nane?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Abisalomu nafika kwa mfumu nati, Onani, ine mnyamata, wanu ndiri nao osenga nkhosa; inu mfumu ndi anyamata anu mupite nane mnyamata wanu.