2 Samuel 13:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Abisalomu adamkakamiza ndithu mpaka Davide adalola kuti Aminoni pamodzi ndi ana onse aamuna a mfumu apite nao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Abisalomu anaiumirira iyo, nilola kuti Aminoni ndi ana amuna onse a mfumu apite naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Abisalomu anamuwumiriza, kotero analola kuti Amnoni pamodzi ndi ana onse a mfumu apite naye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Abisalomu anaiumirira iyo, nilola kuti Amnoni ndi ana amuna onse a mfumu apite naye.