2 Samuel 13:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atamva zimenezi Yonadabu adauza mfumu kuti, “Ana a mfumu abwera. Amfumu, monga momwe ndinakuuzirani muja, ndi m'mene zayendera.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yonadabu ananena ndi mfumu, Onani, ana amuna a mfumu afika; monga ananena mnyamata wanu, momwemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehonadabu anati kwa mfumu, “Taonani ana a mfumu afika. Zachitika monga momwe mtumiki wanu ananenera.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Jonadabu ananena ndi mfumu, Onani, ana amuna a mfumu afika; monga ananena mnyamata wanu, momwemo.