2 Samuel 13:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abisalomu adathaŵa ndithu napita kwa Talimai, mwana wa Amihudi, mfumu ya ku Gesuri. Ndipo Davide adalira maliro a mwana wake Aminoni nthaŵi yaitali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Abisalomu anathawa, nanka kwa Talimai mwana wa Amihudi mfumu ya ku Gesuri. Ndipo Davide analira mwana wake tsiku ndi tsiku.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abisalomu anathawa, napita kwa Talimai mwana wa Amihudi, mfumu ya ku Gesuri. Koma mfumu Davide inalira mwana wake tsiku ndi tsiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Abisalomu anathawa, nanka kwa Talimai mwana wa Amihuri mfumu ya ku Gesuri. Ndipo Davide analira mwana wace tsiku ndi tsiku.