2 Samuel 13:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide adatumiza mau kwa Tamara kuti, “Upite kunyumba kwa mbale wako Aminoni, ukamphikire chakudya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anatumiza mau kwao kwa Tamara, kuti, Upite kunyumba ya mlongo wako Aminoni, numkonzere chakudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anatumiza mawu kwa Tamara ku nyumba yaufumu kuti, “Pita ku nyumba ya mlongo wako Amnoni ndipo ukamukonzere chakudya.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anatumiza mau kwao kwa Tamara, kuti, Upite ku nyumba ya mlongo wako Amnoni, numkonzere cakudya,