2 Samuel 14:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yowabu, mwana wa Zeruya, adaadziŵa kuti mtima wa mfumu uli pa Abisalomu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yowabu mwana wa Zeruya anazindikira kuti mtima wa mfumu unalunjika kwa Abisalomu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yowabu mwana wa Zeruya anadziwa kuti maganizo a mfumu ali pa Abisalomu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoabu mwana wa Zeruya anazindikira kuti mtima wa mfumu unalunjika kwa Abisalomu.