2 Samuel 14:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo mfumu idauza mkazi uja kuti, “Mai, pitani kunyumba kwanu, ndichitapo kanthu ineyo pa nkhaniyi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu inanena ndi mkaziyo, Pita kunyumba yako, ndipo ndidzalamulira za iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inati kwa mkaziyo, “Pitani ku nyumba kwanu ndipo ine ndidzalamula mʼmalo mwanu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu inanena ndi mkaziyo, Pita ku nyumba yako, ndipo ndidzalamulira za iwe.