2 Samuel 15:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ahimaazi, mwana wa Zadoki ndiponso Yonatani, mwana wa Abiyatara, nawonso ali komweko. Ndipo podzera mwa iwowo udzandiwuza zonse zimene udzamve.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onani, ali nao komweko ana amuna ao awiri, Ahimaazi mwana wa Zadoki, ndi Yonatani mwana wa Abiyatara; iwowa muwatumize kuti adzandiuze chilichonse mudzachimva.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana awo awiri, Ahimaazi wa Zadoki, ndi Yonatani mwana wa Abiatara ali nawo pamodzi, uzikawatuma kwa ine ndi china chilichonse chimene ukamve.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onani, ali nao komweko ana amuna ao awiri, Ahimaazi mwana wa Zadoki, ndi Jonatani mwana wa Abyatara; iwowa muwatumize kuti adzandiuze ciri conse mudzacimva.