2 Samuel 15:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo mfumu idamuuza kuti, “Upite ndi mtendere.” Choncho Abisalomu adanyamuka napita ku Hebroni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu inanena naye, Muka ndi mtendere. Chomwecho ananyamuka, nanka ku Hebroni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inati kwa iye, “Pita mu mtendere” Kotero iye anapita ku Hebroni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu inanena naye, Muka ndi mtendere. Comweco ananyamuka, nanka ku Hebroni.