2 Samuel 16:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Davide ndi anthu ake ankayenda mu mseu pamene Simei ankapita mbali inai m'mphepete mwa phiri, kutukwana kuli m'kati. Ndipo ankaponya miyala Davide ndi kumamuwazanso dothi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chomwecho Davide ndi anthu ake anapita m'njira, ndipo Simei analambalala paphiri popenyana naye, namuka natukwana, namponya miyala, nawaza fumbi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero Davide ndi anthu ake anapitirira kuyenda mu msewu pamene Simei amayenda mʼmbali mwa phiri moyangʼanana naye akutukwana ndi kuponya miyala pamene amayenda nʼkumamutsiranso dothi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Comweco Davide ndi anthu ace anapita m'ngra, ndipo Simeyi analambalala paphiri popenyana naye, namuka natukwana, namponya miyala, nawaza pfumbi,