2 Samuel 17:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ife tidzampeza Davide kulikonse kumene adzapezeke, ndipo tidzamthira nkhondo monga m'mene mame amagwera ponseponse pa nthaka. Sipadzapulumuka ndi munthu mmodzi yemwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chomwecho tidamvumbulukira pa malo akuti adzapezeka, ndipo tidzamgwera monga mame agwa panthaka, ndipo sitidzasiya ndi mmodzi yense wa iye ndi anthu onse ali naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ife tidzapita kukamuthira nkhondo kulikonse kumene tikamupeze, ndipo ife tikamuthira nkhondo ngati mame pa nthaka. Palibe amene adzakhale wamoyo kaya iye kapena ankhondo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Comweco tidambvumbulukira pa malo akuti adzapezeka, ndipo tidzamgwera monga mame agwa panthaka, ndipo sitidzasiya ndi mmodzi yense wa iye ndi anthu onse ali naye.