2 Samuel 17:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pompo Davide adanyamukadi pamodzi ndi anthu onse amene anali naye, naoloka mtsinje wa Yordani. Pamene kunkacha, nkuti anthu onse atatha kuwoloka Yordani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomwepo Davide ananyamuka ndi anthu onse amene anali naye, naoloka Yordani. Kutacha m'mawa sanasowe mmodzi wa iwo wosaoloka Yordani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero Davide ndi anthu onse amene anali nawo ananyamuka ndi kuwoloka Yorodani. Pofika mmamawa, panalibe munthu amene anatsala asanawoloke Yorodani!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomwepo Davide ananyamuka ndi anthu onse amene anali naye, naoloka Yordano. Kutaca m'mawa sanasowa mmodzi wa iwo wosaoloka Yordano.