2 Samuel 17:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide atafika ku Mahanaimu, Sobi mwana wa Nahasi Mwamoni wochokera ku Raba, ndi Makiri mwana wa Amiyele wa ku Lodebara, ndiponso Barizilai Mgiliyadi wa ku Rogelimu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali pakufika Davide ku Mahanaimu, Sobi mwana wa Nahasi wa ku Raba wa ana a Amoni, ndi Makiri mwana wa Amiyele wa ku Lodebara, ndi Barizilai Mgiliyadi wa ku Rogelimu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide atafika ku Mahanaimu, Sobi mwana wa Nahasi wochokera ku Raba ku dziko la Amoni ndi Makiri mwana wa Amieli wochokera ku Lodebara, ndi Barizilai Mgiliyadi wochokera ku Rogelimu
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali pakufika Davide ku Mahanaimu, Sobi mwana wa Nahasi wa ku Raba wa ana a Amoni, ndi Makiri mwana wa Amiyeli wa ku Lodebara, ndi Barizilai Mgileadi wa ku Rogelimu,