2 Samuel 17:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
adabwera ndi mabedi ambiri, mabeseni ambiri, ziŵiya zadothi, tirigu, barele, ufa, tirigu wokazinga, nyemba ndi mphodza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
iwo anabwera nao makama, ndi mbale, ndi zotengera zadothi, ndi tirigu, ndi barele, ndi ufa, ndi tirigu wokazinga, ndi nyemba, ndi mphodza, ndi zokazinga zina,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
anabweretsa zofunda, mabeseni ndi miphika. Iwo anabweretsanso kwa Davide ndi anthu ake zakudya izi: tirigu ndi barele, ufa ndi tirigu wokazinga, nyemba ndi mphodza,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iwo anabwera nao makama, ndi mbale, ndi zotengera zadothi, ndi tirigu, ndi barele, ndi ufa, ndi tirigu wokazinga, ndi nyemba, ndi mphodza, ndi zokazinga zina,