2 Samuel 18:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yowabu adauza Mkusi kuti, “Pita, ukauze mfumu zimene waziwonazi.” Mkusiyo adaŵeramira Yowabu mwaulemu, nayamba kuthamanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yowabu ananena ndi Mkusi, Kauze mfumu zimene unaziona. Ndipo Mkusi anawerama kwa Yowabu, nathamanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yowabu anawuza Mkusi kuti, “Pita ukawuze mfumu zimene waona.” Mkusiyo anawerama pamaso pa Yowabu ndipo anathamanga kupita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Yoabu ananena ndi Mkusi, Kauze mfumu zimene unaziona. Ndipo Mkusi anawerama kwa Yoabu, nathamanga.