2 Samuel 18:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo mlondayo adafuula nauza mfumu. Mfumuyo idati, “Ngati ali yekhayekha, ndiye kuti ali ndi nkhani yabwino.” Tsono munthu uja adafika ndithu, nayandikira pafupi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mlondayo anafuula, nauza mfumu. Mfumuyo niti, Ngati ali yekha alikubwera ndi mau. Ndipo iye uja anayenda msanga, nayandikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mlonda uja anapita kwa mfumu ndipo anafotokoza. Mfumu inati, “Ngati ali yekha ali ndi nkhani yabwino” Ndipo munthuyo anayandikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mlondayo anapfuula, nauza mfumu. Mfumuyo niti, Ngati ali yekha alikubwera ndi mau. Ndipo iye uja anayenda msanga, nayandikira.