2 Samuel 18:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumuyo idafunsa Mkusi uja kuti, “Kodi mwana uja Abisalomu zinthu zamuyendera bwino?” Mkusiyo adayankha kuti, “Adani anu mbuyanga mfumu, pamodzi ndi anthu onse amene amakuukirani, ziŵaonekere zomwe zamuwonekera mwanayo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu inanena ndi Mkusiyo, Mnyamatayo Abisalomu ali bwino? Mkusiyo nayankha, Adani a mbuye wanga mfumu, ndi onse akuukira inu kukuchitirani zoipa, akhale monga mnyamata ujayo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inafunsa Mkusiyo kuti, “Kodi mnyamata uja Abisalomu watetezedwa?” Mkusiyo anayankha kuti, “Adani anu mbuye wanga mfumu, pamodzi ndi anthu onse amene amakuwukirani, ziwaonekere zomwe zamuonekera mnyamatayo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu inanena ndi Mkusiyo, Mnyamatayo Abisalomu ali bwino? Mkusiyo nayankha, Adani a mbuye wanga mfumu, ndi onse akuukira inu kukucitirani zoipa, akhale monga mnyamata ujayo.