2 Samuel 19:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Davide adakopa mitima ya Ayuda onse, ndipo adamangana chimodzi. Motero anthuwo adatumiza mau kwa mfumu kuti, “Bwererani inu pamodzi ndi ankhondo anu onse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye anakopa mitima ya anthu onse a Yuda, monga munthu mmodzi, natumiza iwo kwa mfumu, nati, Mubwere inu ndi anyamata anu onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anakopa mitima ya anthu onse a Yuda ndipo anthuwo anakhala ngati munthu mmodzi. Iwo anatumiza mawu kwa mfumu, “Bwererani inu ndi anthu anu onse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anakopa mitima ya anthu onse a Yuda, monga munthu mmodzi, natumiza iwo kwa mfumu, nati, Mubwere inu ndi anyamata anu onse.