2 Samuel 19:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pompo Abisai, mwana wa Zeruya, adafunsa kuti, “Kodi Simeiyu ndiye saphedwa chifukwa chotukwana wodzozedwa wa Chauta?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Abisai mwana wa Zeruya anayankha nati, Kodi sadzaphedwapo Simei chifukwa cha kutemberera wodzozedwa wa Yehova?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Abisai mwana wa Zeruya anati, “Kodi Simei saphedwa chifukwa cha ichi? Iye anatukwana wodzozedwa wa Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Abisai mwana wa Zeruya anayankha nati, Kodi sadzaphedwapo Simeyi cifukwa ca kutemberera wodzozedwa wa Yehova?