2 Samuel 19:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mefiboseti adauza mfumu kuti, “Mloleni mnzangayu kuti atenge ndiye chuma chonsecho. Kwa ine kwakwana kuti inu mbuyanga mfumu mwafika kwanu kuno mwamtendere.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mefiboseti anati kwa mfumu, Lingakhale lonselo alitenge, popeza mbuye wanga mfumu wabwera mumtendere kunyumba yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mefiboseti anati kwa mfumu, “Muloleni atenge zonse, pakuti tsopano mbuye wanga mwafika kwanu mu mtendere.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mefiboseti anati kwa mfumu, Lingakhale lonselo alitenge, popeza mbuye wanga mfumu wabwera mumtendere ku nyumba yace.