2 Samuel 19:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Barizilai adafunsa mfumu kuti, “Kodi ine zanditsalira zaka zingati zokhalabe moyo, kuti ndingapite nanu amfumu ku Yerusalemu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Barizilai ananena ndi mfumu, Masiku a zaka za moyo wanga ndiwo angati, kuti ndiyenera kukwera ndi mfumu kunka ku Yerusalemu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Barizilai anayankha mfumu kuti, “Kodi zakhala zaka zingati zoti ndikhale ndi moyo, kuti ndipite ku Yerusalemu ndi mfumu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Barizilai ananena ndi mfumu, Masiku a zaka za moyo wanga ndiwo angati, kuti ndiyenera kukwera ndi mfumu kumka ku Yerusalemu?