2 Samuel 19:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine mtumiki wanu ndingoyenda pang'ono kuti ndiwoloke Yordani pamodzi ndi inu amfumu. Amfumu mungandipatsirenji mphotho yotere?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mnyamata wanu angofuna kuoloka Yordani pamodzi ndi mfumu; ndipo afuniranji mfumu kundibwezerapo mphotho yotere?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ine mtumiki wanu ndingoyenda pangʼono kuti ndiwoloke Yorodani pamodzi ndi mfumu. Amfumu mungandipatsirenji mphotho yotere?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mnyamata wanu angofuna kuoloka Yordano pamodzi ndi mfumu; ndipo afuniranji mfumu kundibwezerapo mphothoyotere?