2 Samuel 2:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Abinere mwana wa Nere pamodzi ndi ankhondo a Isiboseti mwana wa Saulo adapita ku Gibiyoni kuchokera ku Mahanaimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Abinere mwana wa Nere ndi anyamata a Isiboseti mwana wa Saulo anatuluka ku Mahanaimu kunka ku Gibiyoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abineri mwana wa Neri, pamodzi ndi ankhondo a Isi-Boseti mwana wa Sauli, anachoka ku Mahanaimu ndi kupita ku Gibiyoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Abineri mwana wa Neri ndi anyamata a Isiboseti mwana wa Sauli anaturuka ku Mahanaimu kunka ku Gibeoni.