2 Samuel 2:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abinere adauza Yowabu kuti, “Anyamata anu ndi athu abwere, amenyane tiwone.” Yowabu adati, “Chabwino, namenyane.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Abinere ananena ndi Yowabu, Aimirire anyamata nasewere pamaso pathu. Nati Yowabu, Aimirire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Abineri anati kwa Yowabu, “Tiye tibweretse ena mwa anyamata athu kuti amenyane patsogolo pathupa.” Yowabu anayankha, “Chabwino, amenyane.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Abineri ananena ndi Yoabu, Aimirire anyamata nasewere pamaso pathu. Nati Yoabu, Aimirire.