2 Samuel 2:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anyamatawo adabweradi naŵaŵerenga. A fuko la Benjamini, anyamata a Isiboseti, mwana wa Saulo, analipo khumi ndi aŵiri, anyamata a Davide analinso khumi ndi aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomwepo iwo anaimirira naoloka owerengedwa, khumi ndi awiri a kwa Benjamini, ndi Isiboseti mwana wa Saulo, ndi khumi ndi awiri anyamata a Davide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero anayimirira ndipo anawawerenga: anyamata khumi ndi awiri a fuko la Benjamini ndi Isi-Boseti mwana wa Sauli ndiponso anyamata khumi ndi awiri a Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomwepo iwo anaimirira naoloka owerengedwa, khumi ndi awiri a kwa Benjamini, ndi Isiboseti mwana wa Sauli, ndi khumi ndi awiri a anyamata a Davide.