2 Samuel 2:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono panali nkhondo yoopsa tsiku limenelo. Abinere pamodzi ndi anthu a ku Israele adagonjetsedwa ndi ankhondo a Davide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsikulo nkhondo inakula ndithu. Ndi Abinere ndi anthu a Israele anathawa pamaso pa anyamata a Davide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku limeneli nkhondo yake inali yoopsa kwambiri, ndipo Abineri ndi ankhondo a Israeli anagonjetsedwa ndi ankhondo a Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsikulo nkhondo inakula ndithu. Ndi Abineri ndi anthu a Israyeli anathawa pamaso pa anyamata a Davide.