2 Samuel 2:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Davide adabwera ndi anthu ake aja amene anali nawo, aliyense ndi banja lake. Adakhala m'midzi ya ku Hebroni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anakwera nao anyamata ake okhala naye, munthu yense ndi banja lake; iwowa nakhala m'midzi ya Hebroni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anatenganso anthu amene anali nawo aliyense ndi banja lake, ndipo anakakhala ku midzi ya ku Hebroni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anakwera nao anyamata ace okhala naye, munthu yense ndi banja lace; iwowa nakhala m'midzi ya Hebroni.