2 Samuel 20:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amasayo atachotsedwa pamseupo, anthu onse adatsatira Yowabu, kuti alondole Sheba mwana wa Bikiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atamchotsa iye mumseu, anthu onse anapitirira kumtsata Yowabu kukalondola Sheba mwana wa Bikiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amasa atachotsedwa pa msewu anthu onse anapita ndi Yowabu kuthamangitsa Seba mwana wa Bikiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atamcotsa iye mumseu, anthu onse anapitirira kumsata Yoabu kukalondola Seba mwana wa Bikri.