2 Samuel 20:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ife ndife anthu amtendere ndi okhulupirika m'dziko la Israele. Inu mukufuna kuwononga mzinda umene uli ngati mai m'dziko la Israele. Chifukwa chiyani mukuti mufafanize choloŵa cha Chauta?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine ndine wa awo amene ali amtendere ndi okhulupirika m'Israele; inu mulikufuna kuononga mudzi ndi mai wa m'Israele; mudzamezeranji cholowa cha Yehova?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife ndife anthu a mtendere ndi okhulupirika mu Israeli. Inu mukufuna kuwononga mzinda umene ndi mayi mu Israeli. Nʼchifukwa chiyani mukufuna kufafaniza cholowa cha Yehova?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inendine wa awo amene ali amtendere ndi okhulupirika m'Israyeli; inu mulikufuna kuononga mudzi ndi mai wa m'Israyeli; mudzamezerang colowa ca Yehova?