2 Samuel 20:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Amasa adakaitana Ayuda. Koma adachedwa, napitiriza nthaŵi imene adaamuikira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chomwecho Amasa anamuka kukaitana anthu a Yuda asonkhane; koma anachedwa, napitiriza nthawi imene idamuikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero Amasa anakayitana Ayuda, koma anachedwa, napitirira pa nthawi imene mfumu inamuyikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Comweco Amasa anamuka kukaitana anthu a Yuda asonkhane; koma anacedwa, napitiriza nthawi imene idamuikira.