2 Samuel 20:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Abisai uja, pamodzi ndi ankhondo a Yowabu, ndi Akereti, ndi Apeleti, ndi anyonga onse, adatuluka ku Yerusalemu kumalondola Sheba, mwana wa Bikiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatuluka namtsata anthu a Yowabu, ndi Akereti ndi Apeleti, ndi anthu onse amphamvu; natuluka m'Yerusalemu kukalondola Sheba mwana wa Bikiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero anthu a Yowabu, Akereti ndi Apeleti ndiponso asilikali onse amphamvu anapita motsogozedwa ndi Abisai. Iwo anayenda kuchokera ku Yerusalemu kuthamangitsa Seba mwana wa Bikiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaturuka namtsata anthu a Yoabu, ndi Akereti ndi Apeleti, ndi anthu onseamphamvu; naturuka m'Yerusalemu kukalondola Seba mwana wa Bikri.