2 Samuel 21:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide atamva zimene Rizipa mwana wa Aya, mzikazi wa Saulo adachita,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anauza Davide chimene Rizipa mwana wamkazi wa Aya, mkazi wamng'ono wa Saulo anachita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide atawuzidwa zimene Rizipa mwana wamkazi wa Ayiwa, mzikazi wa Sauli anachita,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anauza Davide cimene Rizipa mwana wamkazi wa Aya, mkazi wamng'ono wa Sauli anacita.