2 Samuel 21:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene iye ankanyoza Aisraele, Yonatani mwana wa Simea, mbale wa Davide, adamupha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakutonza Israele iyeyu, Yonatani mwana a Simea mbale wa Davide anamupha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene iye ankanyoza Aisraeli, Yonatani mwana wa Simea, mʼbale wake wa Davide anamupha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakutonza Israyeli iyeyu, Jonatani mwana wa Simeyi mbale wa Davide anamupha.