2 Samuel 21:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mfumu idasunga Mefiboseti, mwana wa Yonatani, mwana wa Saulo, chifukwa cha kulumbira kumene mfumu Davideyo ndi Yonatani mwana wa Saulo adaachita pamaso pa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mfumu inaleka Mefiboseti mwana wa Yonatani, mwana wa Saulo, chifukwa cha lumbiro la kwa Yehova linali pakati pa Davide ndi Yonatani mwana wa Saulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mfumu inasunga Mefiboseti mwana wa Yonatani, mwana wa Sauli, chifukwa cha kulumbira kumene mfumu Davide ndi Yonatani mwana wa Sauli anachita pamaso pa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mfumu inaleka Mefiboseti mwana wa Jonatani, mwana wa Sauli, cifukwa ca lumbiro la kwa Yehova linali pakati pa Davide ndi Jonatani mwana wa Sauli.