2 Samuel 23:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wotsatana ndi ameneyo anali Sama, mwana wa Age Muharari. Nthaŵi ina Afilisti adasonkhana ku Lehi kumene kunali munda wa mphodza. Aisraele nkuthaŵa Afilisti aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wotsatana naye ndiye Sama mwana wa Age Muharari. Ndipo Afilisti anasonkhana ali gulu pa Lehi pamene panali munda wamphodza; anthu nathawa Afilistiwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wotsatana naye anali Sama mwana wa Age Mharari. Pamene Afilisti anasonkhana pamalo pamene panali munda wa mphodza, ankhondo a Israeli anathawa Afilistiwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo wotsatana naye ndiye Sama mwana wa Age Mharario Ndipo Afilisti anasonkhana ali gulu pamene panali munda wamphodza; anthu nathawa Afilistiwo.