2 Samuel 23:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi yokolola, atatu mwa ankhondo otchuka makumi atatu aja, adapita kwa Davide ku phanga la Adulamu, pamene gulu lankhondo la Afilisti linkamanga zithando zankhondo ku chigwa cha Refaimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atatu a mwa makamu atatu opambanawo, anatsika nafika kwa Davide nyengo ya kukolola m'phanga la ku Adulamu; ndi gulu la Afilisti linamanga zithando m'chigwa cha Refaimu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi yokolola, atatu mwa atsogoleri makumi atatu anabwera kwa Davide ku phanga la Adulamu, pamene gulu la Afilisti linali litamanga misasa mʼchigwa cha Refaimu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atatu a mwamakumi atatu opambanawo, anatsika nafika kwa Davide nyengo ya kukolola m'phanga la ku Adulamu; ndi gulu la Afilisti Gnamanga zithando m'cigwa ca Refaimu.